-
Yeremiya 33:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 “Kodi sunamve zimene anthu awa akunena kuti, ‘Mabanja awiri amene Yehova anawasankha, adzawakanansoʼ? Adani akuchitira anthu anga zinthu zopanda ulemu ndipo sakuwaonanso ngati mtundu wa anthu.
-