26 sindidzakananso mbadwa za Yakobo ndi za Davide mtumiki wanga, kuti pakati pa mbadwa zake ndisatengepo olamulira ana a Abulahamu, Isaki ndi Yakobo. Chifukwa ndidzasonkhanitsa anthu onse amene anatengedwa kupita kudziko lina+ ndipo ndidzawamvera chisoni.’”+