Yeremiya 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinachita pangano ndi makolo anu+ pa tsiku limene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo, kumene anali akapolo.+ Ndinapangana nawo kuti:
13 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinachita pangano ndi makolo anu+ pa tsiku limene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo, kumene anali akapolo.+ Ndinapangana nawo kuti: