-
Yeremiya 34:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Anthuwa ndi akalonga a Yuda, akalonga a Yerusalemu, nduna zapanyumba ya mfumu, ansembe ndi anthu onse amʼdzikoli amene anadutsa pakati pa mwana wa ngʼombe yemwe anamudula pakati.
-