Yeremiya 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Pita kunyumba ya Arekabu,+ ukalankhule nawo ndipo ukabwere nawo kunyumba ya Yehova. Ukalowe nawo mʼchimodzi mwa zipinda zodyera ndipo ukawapatse vinyo kuti amwe.”
2 “Pita kunyumba ya Arekabu,+ ukalankhule nawo ndipo ukabwere nawo kunyumba ya Yehova. Ukalowe nawo mʼchimodzi mwa zipinda zodyera ndipo ukawapatse vinyo kuti amwe.”