-
Yeremiya 35:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako ndinaika makapu ndi zipanda zodzaza ndi vinyo pamaso pa Arekabu nʼkuwauza kuti: “Imwani vinyoyu.”