-
Yeremiya 35:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Musamamange nyumba, musamafese mbewu komanso musamadzale kapena kukhala ndi minda ya mpesa. Koma nthawi zonse muzikhala mʼmatenti kuti mukhale ndi moyo wautali mʼdziko limene mukukhala ngati alendo.’
-