-
Yeremiya 35:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho ife tikupitiriza kumvera mawu a Yehonadabu mwana wa Rekabu kholo lathu, pa chilichonse chimene anatilamula. Timachita zimenezi popewa kumwa vinyo aliyense, ifeyo, akazi athu, ana athu aamuna ndi ana athu aakazi.
-