-
Yeremiya 35:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 “Choncho Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Tsopano Yuda ndi anthu onse amene akukhala mu Yerusalemu ndiwagwetsera masoka onse amene ndinawachenjeza kuti ndidzawagwetsera.+ Ndichita zimenezi chifukwa ndakhala ndikulankhula nawo koma sanandimvere. Ndinkawaitana koma sanandiyankhe.’”+
-