-
Yeremiya 35:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno Yeremiya anauza anthu a mʼnyumba ya Rekabu kuti: “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti mwamvera lamulo la kholo lanu Yehonadabu ndipo mukupitiriza kusunga malamulo ake onse komanso kuchita zonse zimene anakulamulani,
-