Yeremiya 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwina anthu a mʼnyumba ya Yuda akamva za masoka onse amene ndikufuna kuwagwetsera, adzabwerera nʼkusiya njira zawo zoipa. Akatero, ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndi machimo awo.”+
3 Mwina anthu a mʼnyumba ya Yuda akamva za masoka onse amene ndikufuna kuwagwetsera, adzabwerera nʼkusiya njira zawo zoipa. Akatero, ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndi machimo awo.”+