-
Yeremiya 36:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Yeremiya anauza Baruki kuti: “Ine anditsekera ndipo sindingathe kukalowa mʼnyumba ya Yehova.