-
Yeremiya 36:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho iweyo ndi amene ukuyenera kupita kukawerenga mokweza mawu a Yehova amene ali mumpukutu umene ndakuuza kuti ulembe. Ukawerenge mokweza pamaso pa anthu onse mʼnyumba ya Yehova pa tsiku losala kudya. Ukakatero ukakhala kuti wawerengera anthu onse a ku Yuda amene abwera kuchokera mʼmizinda yawo.
-