-
Yeremiya 36:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mwina Yehova adzamva pempho lawo lakuti awakomere mtima ndipo aliyense adzabwerera nʼkusiya njira yake yoipa, popeza Yehova wanena kuti adzasonyeza anthu awa mkwiyo wake ndi ukali wake waukulu.”
-