Yeremiya 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Baruki mwana wa Neriya anachita zonse zimene mneneri Yeremiya anamulamula, kuti apite kunyumba ya Yehova kukawerenga mokweza mawu a Yehova amene analembedwa mumpukutumo.+
8 Choncho Baruki mwana wa Neriya anachita zonse zimene mneneri Yeremiya anamulamula, kuti apite kunyumba ya Yehova kukawerenga mokweza mawu a Yehova amene analembedwa mumpukutumo.+