-
Yeremiya 36:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Zitatero, akalonga onse anatumiza Yehudi mwana wa Netaniya, mwana wa Selemiya, mwana wa Kusa, kukaitana Baruki kuti: “Bwera kuno ndipo utenge mpukutu umene unawerenga mokweza pamaso pa anthu onse.” Choncho Baruki mwana wa Neriya anatenga mpukutuwo nʼkupita nawo kwa iwo.
-