-
Yeremiya 36:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiyeno atamva mawu onsewa anayangʼanana mwamantha, ndipo anauza Baruki kuti: “Ndithu, tikuyenera kukauza mfumu mawu amenewa.”
-