-
Yeremiya 36:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako anafunsa Baruki kuti: “Tiuze, zatheka bwanji kuti ulembe mawu onsewa. Kodi amachita kukuuza?”