-
Yeremiya 36:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kenako akalongawo anapita kwa mfumu mʼbwalo la mkati nʼkusiya mpukutuwo mʼchipinda cha Elisama mlembi ndipo anauza mfumu zonse zimene anamva.
-