Yeremiya 36:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu itamva zimenezi inatuma Yehudi+ kuti akatenge mpukutuwo ndipo iye anakautenga mʼchipinda cha Elisama mlembi. Yehudi anayamba kuwerenga mokweza mpukutuwo pamaso pa mfumu ndi akalonga onse amene anaimirira pafupi ndi mfumuyo.
21 Mfumu itamva zimenezi inatuma Yehudi+ kuti akatenge mpukutuwo ndipo iye anakautenga mʼchipinda cha Elisama mlembi. Yehudi anayamba kuwerenga mokweza mpukutuwo pamaso pa mfumu ndi akalonga onse amene anaimirira pafupi ndi mfumuyo.