Yeremiya 36:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa nthawiyi nʼkuti mfumu ili mʼnyumba imene inkakhala mʼnyengo yozizira ndipo inkawotha moto wamʼmbaula. Umenewu unali mwezi wa 9.*
22 Pa nthawiyi nʼkuti mfumu ili mʼnyumba imene inkakhala mʼnyengo yozizira ndipo inkawotha moto wamʼmbaula. Umenewu unali mwezi wa 9.*