Yeremiya 36:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumu itawotcha mpukutu umene unali ndi mawu amene Baruki analemba atauzidwa ndi Yeremiya, Yehova analankhulanso ndi Yeremiya+ kuti:
27 Mfumu itawotcha mpukutu umene unali ndi mawu amene Baruki analemba atauzidwa ndi Yeremiya, Yehova analankhulanso ndi Yeremiya+ kuti: