Yeremiya 36:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Tenga mpukutu wina ndipo ulembemo mawu onse amene anali mumpukutu woyamba uja, umene Yehoyakimu mfumu ya Yuda wawotcha.+
28 “Tenga mpukutu wina ndipo ulembemo mawu onse amene anali mumpukutu woyamba uja, umene Yehoyakimu mfumu ya Yuda wawotcha.+