30 Choncho ponena za chilango chimene adzapatse Yehoyakimu mfumu ya Yuda, Yehova wanena kuti, ‘Sipadzapezeka mwana wake aliyense wokhala pampando wachifumu wa Davide+ ndipo mtembo wake udzakhala padzuwa lotentha masana ndipo usiku udzakhala panja pozizira.+