Yeremiya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Akasidi adzabweranso kudzamenyana ndi mzinda uno, adzaulanda nʼkuuwotcha ndi moto.”+