-
Yeremiya 37:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Yehova wanena kuti: “Musadzipusitse ponena kuti, ‘Akasidi samenyana nafe, ndithu abwerera,’ chifukwa sachoka ayi.
-