-
Yeremiya 37:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma mneneri Yeremiya atafika pa Geti la Benjamini, mkulu wa alonda amene dzina lake linali Iriya mwana wa Selemiya, mwana wa Hananiya, anamugwira nʼkunena kuti: “Ukuthawira kwa Akasidi iwe!”
-