-
Yeremiya 37:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Yeremiya anamuyankha kuti: “Zabodza zimenezo! Ine sindikuthawira kwa Akasidi.” Koma Iriya sanamumvere. Choncho Iriya anagwira Yeremiya nʼkumupititsa kwa akalonga.
-