Yeremiya 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yeremiya anamuika mʼndende yapansi,* muselo ndipo anakhala mmenemo kwa masiku ambiri.