-
Yeremiya 37:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Yeremiya anafunsanso Mfumu Zedekiya kuti: “Kodi ineyo ndakulakwirani chiyani pamodzi ndi atumiki anu ndiponso anthuwa, kuti munditsekere mʼndende?
-