Yeremiya 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngati simudzadzipereka mʼmanja mwa akalonga* a mfumu ya Babulo, mzindawu udzaperekedwa mʼmanja mwa Akasidi ndipo adzauwotcha ndi moto.+ Inuyo simudzathawa mʼmanja mwawo.’”+
18 Koma ngati simudzadzipereka mʼmanja mwa akalonga* a mfumu ya Babulo, mzindawu udzaperekedwa mʼmanja mwa Akasidi ndipo adzauwotcha ndi moto.+ Inuyo simudzathawa mʼmanja mwawo.’”+