Yeremiya 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mʼchaka cha 9 cha ulamuliro wa Mfumu Zedekiya ya Yuda, mʼmwezi wa 10, Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo ndi asilikali ake onse anafika ku Yerusalemu nʼkuzungulira mzindawo.+
39 Mʼchaka cha 9 cha ulamuliro wa Mfumu Zedekiya ya Yuda, mʼmwezi wa 10, Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo ndi asilikali ake onse anafika ku Yerusalemu nʼkuzungulira mzindawo.+