Yeremiya 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumu Zedekiya ya Yuda ndi asilikali onse ataona adaniwo, anathawira+ kunja kwa mzinda usiku. Iwo anadzera njira yakumunda wa mfumu nʼkukadutsa pageti limene linali pakati pa makoma awiri ndipo anapitiriza kuthawa kulowera ku Araba.+
4 Mfumu Zedekiya ya Yuda ndi asilikali onse ataona adaniwo, anathawira+ kunja kwa mzinda usiku. Iwo anadzera njira yakumunda wa mfumu nʼkukadutsa pageti limene linali pakati pa makoma awiri ndipo anapitiriza kuthawa kulowera ku Araba.+