Yeremiya 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Mutenge uzimuyangʼanira ndipo usamuchitire choipa chilichonse. Koma uzimupatsa chilichonse chimene iye wapempha.”+
12 “Mutenge uzimuyangʼanira ndipo usamuchitire choipa chilichonse. Koma uzimupatsa chilichonse chimene iye wapempha.”+