Yeremiya 39:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu ndi Nebusazibani amene anali Rabisarisi,* Nerigali-sarezera amene anali Rabimagi* ndi akuluakulu onse a mfumu ya Babulo anatuma anthu.
13 Choncho Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu ndi Nebusazibani amene anali Rabisarisi,* Nerigali-sarezera amene anali Rabimagi* ndi akuluakulu onse a mfumu ya Babulo anatuma anthu.