Yeremiya 39:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya mʼBwalo la Alonda+ nʼkumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake. Choncho Yeremiya anayamba kukhala ndi anthu.
14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya mʼBwalo la Alonda+ nʼkumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake. Choncho Yeremiya anayamba kukhala ndi anthu.