-
Yeremiya 41:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma pakati pa anthuwo panali amuna 10 amene anauza Isimaeli kuti: “Usatiphe chifukwa tili ndi nkhokwe za tirigu, barele, mafuta ndi uchi zimene tinazibisa mʼmunda.” Choncho Isimaeli anawasiya ndipo sanawaphe ngati mmene anachitira ndi abale awo.
-