Yeremiya 41:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anakakhala kumalo ogona alendo a Chimamu pafupi ndi Betelehemu+ nʼcholinga choti apitirize ulendo wopita ku Iguputo.+
17 Iwo anakakhala kumalo ogona alendo a Chimamu pafupi ndi Betelehemu+ nʼcholinga choti apitirize ulendo wopita ku Iguputo.+