Yeremiya 42:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musachite mantha ndi mfumu ya Babulo imene mukuiopayo.’+ ‘Mfumu imeneyi musachite nayo mantha, chifukwa ine ndili ndi inu kuti ndikupulumutseni ndi kukulanditsani mʼmanja mwake,’ akutero Yehova.
11 Musachite mantha ndi mfumu ya Babulo imene mukuiopayo.’+ ‘Mfumu imeneyi musachite nayo mantha, chifukwa ine ndili ndi inu kuti ndikupulumutseni ndi kukulanditsani mʼmanja mwake,’ akutero Yehova.