Yeremiya 42:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo ine ndakuuzani lero, koma inu simumvera mawu a Yehova Mulungu wanu kapena kuchita chilichonse chimene wandituma kuti ndidzakuuzeni.+
21 Ndipo ine ndakuuzani lero, koma inu simumvera mawu a Yehova Mulungu wanu kapena kuchita chilichonse chimene wandituma kuti ndidzakuuzeni.+