Yeremiya 43:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatenga amuna, akazi, ana, ana aakazi a mfumu ndiponso aliyense amene Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya mʼmanja mwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani.+ Anatenganso mneneri Yeremiya ndi Baruki mwana wa Neriya. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:6 Nsanja ya Olonda,8/15/2006, tsa. 19
6 Anatenga amuna, akazi, ana, ana aakazi a mfumu ndiponso aliyense amene Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya mʼmanja mwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani.+ Anatenganso mneneri Yeremiya ndi Baruki mwana wa Neriya.