-
Yeremiya 44:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tsopano Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani mukudziitanira tsoka lalikulu? Kodi simukudziwa kuti muphetsa amuna, akazi, ana ndi ana aangʼono mu Yuda, moti sipapezeka aliyense wotsala?
-