Yeremiya 44:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sanadzichepetse* mpaka lero, sanasonyeze mantha aliwonse+ kapena kutsatira malamulo ndi malangizo anga amene ndinapatsa inu ndi makolo anu.’+
10 Iwo sanadzichepetse* mpaka lero, sanasonyeze mantha aliwonse+ kapena kutsatira malamulo ndi malangizo anga amene ndinapatsa inu ndi makolo anu.’+