Yeremiya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma iwe ukufunafuna* zinthu zazikulu. Leka kufunafuna zinthu zimenezo.”’ ‘Chifukwa ndatsala pangʼono kubweretsa tsoka pa anthu onse+ ndipo iwe ndidzakupatsa moyo wako* kuti ukhale mphoto yako kulikonse kumene ungapite,’+ akutero Yehova.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:5 Yeremiya, ptsa. 103-113 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, ptsa. 8-94/15/2008, tsa. 158/15/2006, ptsa. 17-1910/1/2002, ptsa. 14-152/15/2000, tsa. 68/15/1997, tsa. 21 Galamukani!,4/8/2003, tsa. 19
5 Koma iwe ukufunafuna* zinthu zazikulu. Leka kufunafuna zinthu zimenezo.”’ ‘Chifukwa ndatsala pangʼono kubweretsa tsoka pa anthu onse+ ndipo iwe ndidzakupatsa moyo wako* kuti ukhale mphoto yako kulikonse kumene ungapite,’+ akutero Yehova.”
45:5 Yeremiya, ptsa. 103-113 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, ptsa. 8-94/15/2008, tsa. 158/15/2006, ptsa. 17-1910/1/2002, ptsa. 14-152/15/2000, tsa. 68/15/1997, tsa. 21 Galamukani!,4/8/2003, tsa. 19