Yeremiya 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Awa ndi mawu amene Yehova anauza mneneri Yeremiya okhudza mitundu ya anthu:+