-
Yeremiya 47:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Abambo adzathawa osayangʼana mʼmbuyo kuti apulumutse ana awo.
Adzachita zimenezi chifukwa manja awo adzafooka,
Akadzamva mgugu wa mahatchi a adani awo,
Akadzamva phokoso la magaleta ankhondo a adani awo
Komanso kulira kwa mawilo ake,
-