Yeremiya 48:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Perekani chizindikiro chapamsewu kwa anthu a ku Mowabu,Chifukwa adzathawa pamene dziko lawo likusanduka bwinja,Ndipo mizinda yake idzakhala chinthu chochititsa mantha,Moti simudzapezeka aliyense wokhalamo.+
9 Perekani chizindikiro chapamsewu kwa anthu a ku Mowabu,Chifukwa adzathawa pamene dziko lawo likusanduka bwinja,Ndipo mizinda yake idzakhala chinthu chochititsa mantha,Moti simudzapezeka aliyense wokhalamo.+