Yeremiya 48:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsoka la Amowabu lili pafupi,Ndipo nthawi yoti agonjetsedwe ikuyandikira mofulumira kwambiri.+