-
Yeremiya 48:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 “‘Ine ndikudziwa za mkwiyo wake,’ akutero Yehova,
‘Koma mawu ake opanda pakewo sadzakwaniritsidwa.
Iwo sadzachita chilichonse.
-