-
Yeremiya 48:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ndidzachititsa kuti mʼdziko la Mowabu musapezeke
Munthu aliyense wobweretsa nsembe kumalo okwezeka
Komanso munthu wopereka nsembe kwa mulungu wake,’ akutero Yehova.
-